Ekisodo 25:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Uza ana a Isiraeli kuti apereke zopereka kwa ine. Anthu inu mulandire zopereka zanga kwa munthu aliyense amene mtima wake wamulimbikitsa.+ Ekisodo 36:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pamenepo Mose anaitana Bezaleli, Oholiabu ndi mwamuna aliyense wa mtima wanzeru amene Yehova anaika nzeru mumtima mwake.+ Anaitana aliyense amene anali ndi mtima wofunitsitsa kugwira ntchitoyi.+ 2 Akorinto 8:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Mphatso yochokera pansi pa mtima ndi imene Mulungu amakondwera nayo, chifukwa Mulungu amafuna kuti munthu apereke zimene angathe,+ osati zimene sangathe. 2 Akorinto 9:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Aliyense achite mogwirizana ndi mmene watsimikizira mumtima mwake, osati monyinyirika+ kapena mokakamizika, chifukwa Mulungu amakonda munthu wopereka mokondwera.+
2 “Uza ana a Isiraeli kuti apereke zopereka kwa ine. Anthu inu mulandire zopereka zanga kwa munthu aliyense amene mtima wake wamulimbikitsa.+
2 Pamenepo Mose anaitana Bezaleli, Oholiabu ndi mwamuna aliyense wa mtima wanzeru amene Yehova anaika nzeru mumtima mwake.+ Anaitana aliyense amene anali ndi mtima wofunitsitsa kugwira ntchitoyi.+
12 Mphatso yochokera pansi pa mtima ndi imene Mulungu amakondwera nayo, chifukwa Mulungu amafuna kuti munthu apereke zimene angathe,+ osati zimene sangathe.
7 Aliyense achite mogwirizana ndi mmene watsimikizira mumtima mwake, osati monyinyirika+ kapena mokakamizika, chifukwa Mulungu amakonda munthu wopereka mokondwera.+