-
Ekisodo 36:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Ndipo onse a mtima wanzeru+ amene anali kuchita ntchitoyo anayamba kupanga chihema chopatulika,+ nsalu 10 zopetapo akerubi zophimba chihemacho, zopangidwa ndi ulusi wopota wabwino kwambiri, ulusi wabuluu, ubweya wa nkhosa wonyika mu utoto wofiirira ndi ulusi wofiira kwambiri. Iye* anapanga zonsezi.
-