Ekisodo 39:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Ndipo Mose ataona ntchito yonse, anaona kuti achita zonse monga mmene Yehova analamulira. Iwo anachitadi momwemo. Pamenepo Mose anawadalitsa.+ Deuteronomo 4:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Musawonjezepo kalikonse pa mawu amene ndikukulamulani, ndipo musachotsepo kalikonse pa mawu amenewa,+ kuti musunge malamulo a Yehova Mulungu wanu amene ndikukupatsani.
43 Ndipo Mose ataona ntchito yonse, anaona kuti achita zonse monga mmene Yehova analamulira. Iwo anachitadi momwemo. Pamenepo Mose anawadalitsa.+
2 Musawonjezepo kalikonse pa mawu amene ndikukulamulani, ndipo musachotsepo kalikonse pa mawu amenewa,+ kuti musunge malamulo a Yehova Mulungu wanu amene ndikukupatsani.