Ekisodo 9:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 dziwa kuti, dzanja la Yehova+ lipha ziweto zanu zonse.+ Mliri waukulu kwambiri ugwera mahatchi,* abulu, ngamila, ng’ombe ndi nkhosa.+ Ekisodo 11:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Choncho Yehova anauza Mose kuti: “Patsala mliri umodzi wokha woti ndikanthe nawo Farao ndi Iguputo. Kenako adzakulolani kuchoka m’dziko lino.+ Pokulolani kuchoka ndi zonse zimene muli nazo, adzachita kukupitikitsani.+ Ekisodo 12:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Nthawi yomweyo Farao anaitanitsa+ Mose ndi Aroni usiku, ndipo anati: “Nyamukani, chokani pakati pa anthu anga, inuyo ndi ana onse a Isiraeli. Pitani, katumikireni Yehova, monga momwe mwanenera.+
3 dziwa kuti, dzanja la Yehova+ lipha ziweto zanu zonse.+ Mliri waukulu kwambiri ugwera mahatchi,* abulu, ngamila, ng’ombe ndi nkhosa.+
11 Choncho Yehova anauza Mose kuti: “Patsala mliri umodzi wokha woti ndikanthe nawo Farao ndi Iguputo. Kenako adzakulolani kuchoka m’dziko lino.+ Pokulolani kuchoka ndi zonse zimene muli nazo, adzachita kukupitikitsani.+
31 Nthawi yomweyo Farao anaitanitsa+ Mose ndi Aroni usiku, ndipo anati: “Nyamukani, chokani pakati pa anthu anga, inuyo ndi ana onse a Isiraeli. Pitani, katumikireni Yehova, monga momwe mwanenera.+