Genesis 17:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Pamene Abulamu anali ndi zaka 99, Yehova anaonekera kwa iye n’kumuuza kuti:+ “Ine ndine Mulungu Wamphamvuyonse.+ Yenda pamaso panga ndipo ukhale wolungama.+ Genesis 35:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mulungu anamuuzanso kuti: “Ine ndine Mulungu Wamphamvuyonse.+ Ubereke ndipo ukhale ndi ana ambiri. Mitundu ndi mafuko ambiri adzatuluka mwa iwe, ndipo mafumu adzatuluka m’chiuno mwako.+
17 Pamene Abulamu anali ndi zaka 99, Yehova anaonekera kwa iye n’kumuuza kuti:+ “Ine ndine Mulungu Wamphamvuyonse.+ Yenda pamaso panga ndipo ukhale wolungama.+
11 Mulungu anamuuzanso kuti: “Ine ndine Mulungu Wamphamvuyonse.+ Ubereke ndipo ukhale ndi ana ambiri. Mitundu ndi mafuko ambiri adzatuluka mwa iwe, ndipo mafumu adzatuluka m’chiuno mwako.+