Salimo 41:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Yehova adzamuteteza ndi kumusunga ali wamoyo.+Adzatchedwa wodala padziko lapansi.+Ndipo Mulungu sangamupereke kwa adani ake.+ Miyambo 11:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Munthu woipa amapeza malipiro achinyengo,+ koma wofesa chilungamo amapeza malipiro enieni.+ Miyambo 19:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Wokomera mtima munthu wonyozeka akukongoza Yehova,+ ndipo adzam’bwezera zimene anachitazo.+ Mlaliki 8:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ngakhale woipa atachita zoipa+ maulendo 100 n’kukhala ndi moyo wautali akuchitabe zofuna zake, ine ndikudziwa kuti anthu amene amaopa Mulungu woona zidzawayendera bwino,+ chifukwa chakuti anali kumuopa.+ Yesaya 3:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Amuna inu, nenani kuti anthu olungama zidzawayendera bwino,+ chifukwa adzadya zipatso za zochita zawo.+ Luka 1:50 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 50 Chifundo chake chakhala pa amene amamuopa ku mibadwomibadwo.+ Aheberi 6:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pakuti Mulungu si wosalungama woti angaiwale ntchito yanu ndi chikondi chimene munachisonyeza pa dzina lake,+ mwa kutumikira oyera+ ndipo mukupitiriza kuwatumikira.
2 Yehova adzamuteteza ndi kumusunga ali wamoyo.+Adzatchedwa wodala padziko lapansi.+Ndipo Mulungu sangamupereke kwa adani ake.+
12 Ngakhale woipa atachita zoipa+ maulendo 100 n’kukhala ndi moyo wautali akuchitabe zofuna zake, ine ndikudziwa kuti anthu amene amaopa Mulungu woona zidzawayendera bwino,+ chifukwa chakuti anali kumuopa.+
10 Amuna inu, nenani kuti anthu olungama zidzawayendera bwino,+ chifukwa adzadya zipatso za zochita zawo.+
10 Pakuti Mulungu si wosalungama woti angaiwale ntchito yanu ndi chikondi chimene munachisonyeza pa dzina lake,+ mwa kutumikira oyera+ ndipo mukupitiriza kuwatumikira.