Ekisodo 24:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndiyeno anatenga buku la pangano+ ndi kuwerengera anthuwo kuti amve.+ Zitatero anthuwo anati: “Zonse zimene Yehova wanena tidzachita zomwezo ndipo tidzamumvera.”+ Deuteronomo 26:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Inu lero mwachititsa Yehova kunena kuti adzakhala Mulungu wanu mukamayenda m’njira zake ndi kusunga malangizo,+ malamulo+ ndi zigamulo zake+ ndiponso kumvera mawu ake.+ Yoswa 24:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ndiyeno anthuwo anamuyankha Yoswa kuti: “Tizitumikira Yehova Mulungu wathu ndi kumvera mawu ake!”+
7 Ndiyeno anatenga buku la pangano+ ndi kuwerengera anthuwo kuti amve.+ Zitatero anthuwo anati: “Zonse zimene Yehova wanena tidzachita zomwezo ndipo tidzamumvera.”+
17 Inu lero mwachititsa Yehova kunena kuti adzakhala Mulungu wanu mukamayenda m’njira zake ndi kusunga malangizo,+ malamulo+ ndi zigamulo zake+ ndiponso kumvera mawu ake.+
24 Ndiyeno anthuwo anamuyankha Yoswa kuti: “Tizitumikira Yehova Mulungu wathu ndi kumvera mawu ake!”+