Numeri 8:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Aleviwo anadziyeretsa+ n’kuchapa zovala zawo. Pambuyo pake, Aroni anawauza kuti ayende uku ndi uku monga nsembe yoweyula pamaso pa Yehova.+ Kenako Aroniyo anawaphimbira machimo awo kuti awayeretse.+
21 Aleviwo anadziyeretsa+ n’kuchapa zovala zawo. Pambuyo pake, Aroni anawauza kuti ayende uku ndi uku monga nsembe yoweyula pamaso pa Yehova.+ Kenako Aroniyo anawaphimbira machimo awo kuti awayeretse.+