Ekisodo 25:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 “Kenako upange choikapo nyale chagolide woyenga bwino. Chimenechi chikhale chosula.+ Choikapo nyalecho chikhale ndi tsinde, nthambi, masamba ofunga duwa, mfundo ndi maluwa. Yeremiya 52:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Mkulu wa asilikali olondera mfumu uja anatenga mabeseni,+ zopalira moto, mbale zolowa,+ ndowa zochotsera phulusa, zoikapo nyale,+ zikho ndi mbale zinanso zolowa zomwe zinali zagolide weniweni,+ komanso zomwe zinali zasiliva weniweni.+ Aheberi 9:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pakuti panamangidwa chipinda choyamba cha chihema.+ M’chipindamo munali choikapo nyale,+ tebulo,+ ndi mitanda ya mkate woonetsedwa,+ ndipo chinali kutchedwa “Malo Oyera.”+
31 “Kenako upange choikapo nyale chagolide woyenga bwino. Chimenechi chikhale chosula.+ Choikapo nyalecho chikhale ndi tsinde, nthambi, masamba ofunga duwa, mfundo ndi maluwa.
19 Mkulu wa asilikali olondera mfumu uja anatenga mabeseni,+ zopalira moto, mbale zolowa,+ ndowa zochotsera phulusa, zoikapo nyale,+ zikho ndi mbale zinanso zolowa zomwe zinali zagolide weniweni,+ komanso zomwe zinali zasiliva weniweni.+
2 Pakuti panamangidwa chipinda choyamba cha chihema.+ M’chipindamo munali choikapo nyale,+ tebulo,+ ndi mitanda ya mkate woonetsedwa,+ ndipo chinali kutchedwa “Malo Oyera.”+