-
Yeremiya 32:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Ndiyeno Hanameli mwana wa m’bale wa bambo anga analowa m’Bwalo la Alonda+ ndipo anandipeza mogwirizana ndi mawu a Yehova. Pamenepo iye anati: “Gula munda wanga wa ku Anatoti,+ m’dziko la Benjamini,+ pakuti iweyo ndi amene uli ndi ufulu woulandira monga cholowa ndiponso uli ndi ufulu wougula. Uugule ndithu.” Atatero ndinadziwa kuti mawu amenewa anali a Yehova.+
-