Levitiko 25:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Muzisunga malangizo anga ndi zigamulo zanga. Mukatero mudzakhala otetezeka m’dzikolo.+ Miyambo 1:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Koma munthu wondimvera adzakhala mwabata+ ndipo sadzasokonezeka chifukwa choopa tsoka.”+ Yeremiya 23:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 M’masiku a mfumu imeneyi, Yuda adzapulumutsidwa,+ ndipo Isiraeli adzakhala mwabata.+ Dzina la mfumuyi lidzakhala Yehova Ndiye Chilungamo Chathu.”+
6 M’masiku a mfumu imeneyi, Yuda adzapulumutsidwa,+ ndipo Isiraeli adzakhala mwabata.+ Dzina la mfumuyi lidzakhala Yehova Ndiye Chilungamo Chathu.”+