-
Yoswa 22:19Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
19 Ngati n’zoona kuti dziko lanu n’lodetsedwa,+ wolokerani kudziko la Yehova+ kumene kuli chihema chopatulika cha Yehova,+ mukakhazikike pakati pathu. Koma musapandukire Yehova, ndipo musachititse ifeyo kupanduka chifukwa cha guwa lansembe limene mwamangali, kuwonjezera pa guwa lansembe la Yehova Mulungu wathu.+
-