Ekisodo 6:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Chotero ndidzakutengani kukhala anthu anga,+ ndi kukusonyezani kuti ndine Mulungu.+ Inuyo mudzadziwadi kuti ine ndine Yehova Mulungu wanu, amene ndidzakutulutsani mu Iguputo, ndi kukuchotserani goli lawo.+ Deuteronomo 23:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Pakuti Yehova Mulungu wanu akuyendayenda mumsasa wanu kuti akulanditseni+ ndi kupereka adani anu m’manja mwanu.+ Choncho msasa wanu uzikhala woyera,+ kuti asaone choipa chilichonse pakati panu ndi kutembenuka n’kuleka kuyenda nanu limodzi.+ 2 Akorinto 6:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ndipo pali kumvana kotani pakati pa kachisi wa Mulungu ndi mafano?+ Pakuti ifeyo ndife kachisi+ wa Mulungu wamoyo, monga ananenera Mulungu kuti: “Ndidzakhala pakati pawo+ ndi kuyenda pakati pawo. Ndidzakhala Mulungu wawo, ndipo iwo adzakhala anthu anga.”+
7 Chotero ndidzakutengani kukhala anthu anga,+ ndi kukusonyezani kuti ndine Mulungu.+ Inuyo mudzadziwadi kuti ine ndine Yehova Mulungu wanu, amene ndidzakutulutsani mu Iguputo, ndi kukuchotserani goli lawo.+
14 Pakuti Yehova Mulungu wanu akuyendayenda mumsasa wanu kuti akulanditseni+ ndi kupereka adani anu m’manja mwanu.+ Choncho msasa wanu uzikhala woyera,+ kuti asaone choipa chilichonse pakati panu ndi kutembenuka n’kuleka kuyenda nanu limodzi.+
16 Ndipo pali kumvana kotani pakati pa kachisi wa Mulungu ndi mafano?+ Pakuti ifeyo ndife kachisi+ wa Mulungu wamoyo, monga ananenera Mulungu kuti: “Ndidzakhala pakati pawo+ ndi kuyenda pakati pawo. Ndidzakhala Mulungu wawo, ndipo iwo adzakhala anthu anga.”+