Ezekieli 33:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 “Choncho iwe mwana wa munthu, uza nyumba ya Isiraeli kuti, ‘Anthu inu mwanena kuti: “Tingakhale bwanji ndi moyo, popeza kuti kupanduka kwathu ndi machimo athu zili pa ife ndipo tikuwola+ chifukwa cha zimenezi?”’+
10 “Choncho iwe mwana wa munthu, uza nyumba ya Isiraeli kuti, ‘Anthu inu mwanena kuti: “Tingakhale bwanji ndi moyo, popeza kuti kupanduka kwathu ndi machimo athu zili pa ife ndipo tikuwola+ chifukwa cha zimenezi?”’+