Deuteronomo 11:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Mukatero mkwiyo wa Yehova udzakuyakirani. Adzatseka kumwamba moti mvula sidzagwa+ ndipo nthaka sidzatulutsa zipatso zake. Pamenepo mudzafafanizika mwamsanga m’dziko labwinolo limene Yehova akukupatsani.+ Deuteronomo 28:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 “Chidzakhala chotembereredwa chipatso cha mimba yako,+ chipatso cha nthaka yako,+ ana a ng’ombe zako ndi ana a nkhosa zako.+ Hagai 1:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 ‘N’chifukwa chake kumwamba sikunakugwetsereni mame, ndipo dziko lapansi silinakupatseni zipatso zake.+
17 Mukatero mkwiyo wa Yehova udzakuyakirani. Adzatseka kumwamba moti mvula sidzagwa+ ndipo nthaka sidzatulutsa zipatso zake. Pamenepo mudzafafanizika mwamsanga m’dziko labwinolo limene Yehova akukupatsani.+
18 “Chidzakhala chotembereredwa chipatso cha mimba yako,+ chipatso cha nthaka yako,+ ana a ng’ombe zako ndi ana a nkhosa zako.+
10 ‘N’chifukwa chake kumwamba sikunakugwetsereni mame, ndipo dziko lapansi silinakupatseni zipatso zake.+