Levitiko 3:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 “‘Ngati akupereka nkhosa kapena mbuzi monga nsembe yachiyanjano kwa Yehova, azipereka yamphongo kapena yaikazi, yopanda chilema.+ Aheberi 7:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Pakuti mkulu wa ansembe ngati ameneyu ndiyedi wotiyenerera.+ Iye ndi wokhulupirika,+ wosalakwa,+ wosaipitsidwa,+ wosiyana ndi anthu ochimwa,+ ndipo wakwera pamwamba kwambiri kuposa kumwamba.+ Aheberi 9:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 kuli bwanji magazi+ a Khristu, amene anadzipereka wopanda chilema kwa Mulungu kudzera mwa mzimu wamuyaya?+ Kodi magazi amenewo sadzayeretsa+ zikumbumtima zathu ku ntchito zakufa,+ kuti tichite utumiki wopatulika+ kwa Mulungu wamoyo? 1 Petulo 2:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Iye sanachite tchimo,+ ndipo m’kamwa mwake simunapezeke chinyengo.+
6 “‘Ngati akupereka nkhosa kapena mbuzi monga nsembe yachiyanjano kwa Yehova, azipereka yamphongo kapena yaikazi, yopanda chilema.+
26 Pakuti mkulu wa ansembe ngati ameneyu ndiyedi wotiyenerera.+ Iye ndi wokhulupirika,+ wosalakwa,+ wosaipitsidwa,+ wosiyana ndi anthu ochimwa,+ ndipo wakwera pamwamba kwambiri kuposa kumwamba.+
14 kuli bwanji magazi+ a Khristu, amene anadzipereka wopanda chilema kwa Mulungu kudzera mwa mzimu wamuyaya?+ Kodi magazi amenewo sadzayeretsa+ zikumbumtima zathu ku ntchito zakufa,+ kuti tichite utumiki wopatulika+ kwa Mulungu wamoyo?