Ekisodo 28:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Ndiyeno uike Urimu+ ndi Tumimu m’chovala pachifuwa chachiweruzo, ndipo zizikhala pamtima pa Aroni akamalowa kukaonekera pamaso pa Yehova. Aroni azinyamula ziweruzo+ za ana a Isiraeli pamtima pake poonekera kwa Yehova nthawi zonse. Ezara 2:63 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 63 Pa chifukwa chimenechi, Tirisata*+ anawauza kuti sayenera kudya+ zinthu zopatulika koposa, kufikira patakhala wansembe wokhala ndi Urimu+ ndi Tumimu. Yohane 5:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Ine sindingachite chilichonse chongoganiza ndekha. Ndimaweruza malinga ndi mmene ndamvera, ndipo chiweruzo chimene ndimapereka n’cholungama,+ chifukwa sinditsatira chifuniro changa, koma chifuniro+ cha amene anandituma.
30 Ndiyeno uike Urimu+ ndi Tumimu m’chovala pachifuwa chachiweruzo, ndipo zizikhala pamtima pa Aroni akamalowa kukaonekera pamaso pa Yehova. Aroni azinyamula ziweruzo+ za ana a Isiraeli pamtima pake poonekera kwa Yehova nthawi zonse.
63 Pa chifukwa chimenechi, Tirisata*+ anawauza kuti sayenera kudya+ zinthu zopatulika koposa, kufikira patakhala wansembe wokhala ndi Urimu+ ndi Tumimu.
30 Ine sindingachite chilichonse chongoganiza ndekha. Ndimaweruza malinga ndi mmene ndamvera, ndipo chiweruzo chimene ndimapereka n’cholungama,+ chifukwa sinditsatira chifuniro changa, koma chifuniro+ cha amene anandituma.