2 Akorinto 9:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Aliyense achite mogwirizana ndi mmene watsimikizira mumtima mwake, osati monyinyirika+ kapena mokakamizika, chifukwa Mulungu amakonda munthu wopereka mokondwera.+
7 Aliyense achite mogwirizana ndi mmene watsimikizira mumtima mwake, osati monyinyirika+ kapena mokakamizika, chifukwa Mulungu amakonda munthu wopereka mokondwera.+