Genesis 9:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ndiyeno Hamu,+ bambo wake wa Kanani, anaona maliseche a bambo ake.+ Atatero, anapita panja n’kukauza abale ake awiri aja zimenezo.+ Ezekieli 22:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Anthu avula bambo awo.+ Iwo agona ndi mkazi wodetsedwa amene akusamba.+
22 Ndiyeno Hamu,+ bambo wake wa Kanani, anaona maliseche a bambo ake.+ Atatero, anapita panja n’kukauza abale ake awiri aja zimenezo.+