Levitiko 15:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Mwamuna akagonana ndi mkazi ameneyu, azikhala wodetsedwa chifukwa chakuti mkaziyo akusamba.+ Zikatero, mwamunayo azikhala wodetsedwa masiku 7, ndipo bedi lililonse limene angagonepo lizikhala lodetsedwa. Levitiko 20:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 “‘Mwamuna akagona ndi mkazi amene ali pa nyengo ya kusamba, onse awiri sanalemekeze magazi ake.+ Choncho onse awiri aziphedwa kuti asakhalenso pakati pa anthu awo. Ezekieli 22:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Anthu avula bambo awo.+ Iwo agona ndi mkazi wodetsedwa amene akusamba.+
24 Mwamuna akagonana ndi mkazi ameneyu, azikhala wodetsedwa chifukwa chakuti mkaziyo akusamba.+ Zikatero, mwamunayo azikhala wodetsedwa masiku 7, ndipo bedi lililonse limene angagonepo lizikhala lodetsedwa.
18 “‘Mwamuna akagona ndi mkazi amene ali pa nyengo ya kusamba, onse awiri sanalemekeze magazi ake.+ Choncho onse awiri aziphedwa kuti asakhalenso pakati pa anthu awo.