Levitiko 20:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ndipo musatsatire mfundo za mitundu imene ndikuichotsa pamaso panu,+ chifukwa iwo amachita zonsezi ndipo amandinyansa.+ Deuteronomo 18:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pakuti aliyense wochita zimenezi ndi wonyansa kwa Yehova. Ndipo chifukwa chakuti anthu a mitundu ina akuchita zimenezi, Yehova Mulungu wako akuwapitikitsa pamaso pako.+
23 Ndipo musatsatire mfundo za mitundu imene ndikuichotsa pamaso panu,+ chifukwa iwo amachita zonsezi ndipo amandinyansa.+
12 Pakuti aliyense wochita zimenezi ndi wonyansa kwa Yehova. Ndipo chifukwa chakuti anthu a mitundu ina akuchita zimenezi, Yehova Mulungu wako akuwapitikitsa pamaso pako.+