27 Iye safunikira kupereka tsiku ndi tsiku+ nsembe za machimo ake choyamba,+ kenako za anthu ena, monga mmene amachitira akulu a ansembe.+ (Iye anachita zimenezi kamodzi+ kokha pamene anadzipereka yekha nsembe.+ Nsembe imene anapereka motereyi ithandiza anthu mpaka muyaya.)