Ekisodo 20:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 “Uzilemekeza bambo ako ndi mayi ako+ kuti masiku ako atalike m’dziko limene Yehova Mulungu wako akukupatsa.+ Aefeso 6:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Uzilemekeza bambo ako ndi mayi ako,”+ ndilo lamulo loyamba lokhala ndi lonjezo:+ Aheberi 12:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndiponso, bambo athu otibereka, amene anali ndi thupi lanyama ngati lathuli anali kutilanga,+ ndipo tinali kuwalemekeza. Kuli bwanji ndi Atate wa moyo wathu wauzimu. Kodi sitiyenera kuwagonjera koposa pamenepo kuti tikhale ndi moyo?+
12 “Uzilemekeza bambo ako ndi mayi ako+ kuti masiku ako atalike m’dziko limene Yehova Mulungu wako akukupatsa.+
9 Ndiponso, bambo athu otibereka, amene anali ndi thupi lanyama ngati lathuli anali kutilanga,+ ndipo tinali kuwalemekeza. Kuli bwanji ndi Atate wa moyo wathu wauzimu. Kodi sitiyenera kuwagonjera koposa pamenepo kuti tikhale ndi moyo?+