Levitiko 6:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Monga nsembe yake ya kupalamula, azibweretsa kwa Yehova nkhosa yamphongo yopanda chilema.+ Azipereka kwa wansembe nkhosa ya mtengo wofanana ndi mtengo umene wagamulidwa, kuti ikhale nsembe ya kupalamula.+
6 Monga nsembe yake ya kupalamula, azibweretsa kwa Yehova nkhosa yamphongo yopanda chilema.+ Azipereka kwa wansembe nkhosa ya mtengo wofanana ndi mtengo umene wagamulidwa, kuti ikhale nsembe ya kupalamula.+