Ekisodo 28:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Aroni m’bale wako umupangire zovala zopatulika kuti zimupatse ulemerero ndi kum’kongoletsa.+ Ekisodo 29:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 “Zovala zopatulika+ za Aroni zidzakhala za ana ake+ obwera m’mbuyo mwake. Adzawadzoza+ ndi kuwapatsa mphamvu atavala zovala zimenezi.+ Levitiko 16:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 “Wansembe amene adzadzozedwa+ ndi kupatsidwa mphamvu* kuti atumikire monga wansembe,+ kulowa m’malo+ mwa bambo ake, aziphimba machimo ndipo azivala zovala za nsalu.+ Zovala zimenezo ndi zopatulika.+
29 “Zovala zopatulika+ za Aroni zidzakhala za ana ake+ obwera m’mbuyo mwake. Adzawadzoza+ ndi kuwapatsa mphamvu atavala zovala zimenezi.+
32 “Wansembe amene adzadzozedwa+ ndi kupatsidwa mphamvu* kuti atumikire monga wansembe,+ kulowa m’malo+ mwa bambo ake, aziphimba machimo ndipo azivala zovala za nsalu.+ Zovala zimenezo ndi zopatulika.+