Numeri 16:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Si izi nanga, sunatifikitse kudziko lililonse loyenda mkaka ndi uchi,+ kumene ungatigawire malo ndiponso minda ya mpesa. Kodi ukufuna kuti amunawo uwakolowole maso? Tatitu kumeneko sitibwerako!” Deuteronomo 8:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Mungaiwale amene anakuyendetsani m’chipululu chachikulu ndi chochititsa mantha,+ chokhala ndi njoka zapoizoni,+ zinkhanira ndiponso dziko louma lopanda madzi. Amenenso anakutulutsirani madzi pamwala wolimba ngati nsangalabwi.+ Nehemiya 9:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Kwa zaka 40+ munawapatsa chakudya m’chipululu. Iwo sanasowe kanthu.+ Zovala zawo sizinathe+ ndipo mapazi awo sanatupe.+
14 Si izi nanga, sunatifikitse kudziko lililonse loyenda mkaka ndi uchi,+ kumene ungatigawire malo ndiponso minda ya mpesa. Kodi ukufuna kuti amunawo uwakolowole maso? Tatitu kumeneko sitibwerako!”
15 Mungaiwale amene anakuyendetsani m’chipululu chachikulu ndi chochititsa mantha,+ chokhala ndi njoka zapoizoni,+ zinkhanira ndiponso dziko louma lopanda madzi. Amenenso anakutulutsirani madzi pamwala wolimba ngati nsangalabwi.+
21 Kwa zaka 40+ munawapatsa chakudya m’chipululu. Iwo sanasowe kanthu.+ Zovala zawo sizinathe+ ndipo mapazi awo sanatupe.+