Numeri 1:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 kuchokera ku fuko la Dani,+ Ahiyezeri+ mwana wa Amisadai, Numeri 7:66 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 66 Pa tsiku la 10 panali mtsogoleri wa ana a Dani, Ahiyezeri+ mwana wa Amisadai. Numeri 10:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Pomaliza, a m’chigawo cha mafuko atatu cha ana a Dani+ ananyamuka. Iwo ndiwo anali olonda kumbuyo kwa zigawo zonse za mafukowo.+ Mtsogoleri wa asilikali awo anali Ahiyezeri,+ mwana wa Amisadai.
25 Pomaliza, a m’chigawo cha mafuko atatu cha ana a Dani+ ananyamuka. Iwo ndiwo anali olonda kumbuyo kwa zigawo zonse za mafukowo.+ Mtsogoleri wa asilikali awo anali Ahiyezeri,+ mwana wa Amisadai.