1 Samueli 15:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Kuwonjezera apo, Wolemekezeka wa Isiraeli+ sadzalephera kukwaniritsa mawu ake,+ ndipo sadzadzimva kuti ali ndi mlandu, pakuti Iye si munthu kuti adzimve wamlandu.”+ Aroma 11:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Mulungu sadzadandaula+ chifukwa cha mphatso zake ndiponso chifukwa chakuti anawaitana.
29 Kuwonjezera apo, Wolemekezeka wa Isiraeli+ sadzalephera kukwaniritsa mawu ake,+ ndipo sadzadzimva kuti ali ndi mlandu, pakuti Iye si munthu kuti adzimve wamlandu.”+