Ekisodo 6:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Ndipo Eleazara mwana wa Aroni,+ anatenga mwana wamkazi wa Putieli kukhala mkazi wake. Ndipo iye anam’berekera Pinihasi.+ Amenewa ndiwo atsogoleri a mabanja a m’fuko la Levi, malinga ndi mzere wobadwira wa makolo awo.+ Yoswa 22:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Wansembe Pinihasi,+ atsogoleri a khamu la Aisiraeli+ kapena kuti atsogoleri a masauzande a Aisiraeli amene anali naye, atamva mawu amene ana a Rubeni, ana a Gadi ndi ana a Manase ananena, anakhutira nawo mawuwo. 1 Mbiri 6:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Eleazara+ anabereka Pinihasi,+ Pinihasi anabereka Abisuwa,+
25 Ndipo Eleazara mwana wa Aroni,+ anatenga mwana wamkazi wa Putieli kukhala mkazi wake. Ndipo iye anam’berekera Pinihasi.+ Amenewa ndiwo atsogoleri a mabanja a m’fuko la Levi, malinga ndi mzere wobadwira wa makolo awo.+
30 Wansembe Pinihasi,+ atsogoleri a khamu la Aisiraeli+ kapena kuti atsogoleri a masauzande a Aisiraeli amene anali naye, atamva mawu amene ana a Rubeni, ana a Gadi ndi ana a Manase ananena, anakhutira nawo mawuwo.