Ekisodo 6:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndipo ana a Kohati anali Amuramu, Izara, Heburoni ndi Uziyeli.+ Kohati anakhala ndi moyo zaka 133. Numeri 3:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ana a Kohati,+ malinga ndi mayina a mabanja awo, anali Amuramu, Izara,+ Heburoni ndi Uziyeli.
18 Ndipo ana a Kohati anali Amuramu, Izara, Heburoni ndi Uziyeli.+ Kohati anakhala ndi moyo zaka 133.