Numeri 19:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 “‘Ndiyeno munthu wosadetsedwa awole phulusa+ la ng’ombeyo, akalithire pamalo oyera kunja kwa msasawo. Phulusalo alisunge kuti azilithira m’madzi oyeretsera+ khamu la ana a Isiraeli. Imeneyi ndi nsembe yamachimo.
9 “‘Ndiyeno munthu wosadetsedwa awole phulusa+ la ng’ombeyo, akalithire pamalo oyera kunja kwa msasawo. Phulusalo alisunge kuti azilithira m’madzi oyeretsera+ khamu la ana a Isiraeli. Imeneyi ndi nsembe yamachimo.