Numeri 14:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Inu simudzalowa m’dziko limene ndinachita kukweza dzanja langa+ polumbira kuti ndidzakhala nanu mmenemo, kupatula Kalebe mwana wa Yefune, ndi Yoswa mwana wa Nuni.+ Numeri 26:65 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 65 Zinakhala choncho chifukwa ponena za iwo, Yehova anati: “Mulimonsemo adzafera m’chipululu basi.”+ Choncho, sipanatsale ndi mmodzi yemwe kupatulapo Kalebe mwana wa Yefune, ndi Yoswa mwana wa Nuni.+
30 Inu simudzalowa m’dziko limene ndinachita kukweza dzanja langa+ polumbira kuti ndidzakhala nanu mmenemo, kupatula Kalebe mwana wa Yefune, ndi Yoswa mwana wa Nuni.+
65 Zinakhala choncho chifukwa ponena za iwo, Yehova anati: “Mulimonsemo adzafera m’chipululu basi.”+ Choncho, sipanatsale ndi mmodzi yemwe kupatulapo Kalebe mwana wa Yefune, ndi Yoswa mwana wa Nuni.+