Salimo 26:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Sindinakhale pansi pamodzi ndi anthu achinyengo.+Ndipo sindinayanjane ndi anthu obisa umunthu wawo.+ Miyambo 30:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Nayi njira ya mkazi wachigololo: Iye amadya n’kupukuta pakamwa pake ndipo amanena kuti: “Sindinachite cholakwa chilichonse.”+
4 Sindinakhale pansi pamodzi ndi anthu achinyengo.+Ndipo sindinayanjane ndi anthu obisa umunthu wawo.+
20 Nayi njira ya mkazi wachigololo: Iye amadya n’kupukuta pakamwa pake ndipo amanena kuti: “Sindinachite cholakwa chilichonse.”+