-
Numeri 7:25Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
25 Iye anapereka mbale yaikulu imodzi yasiliva yolemera masekeli 130, ndiponso mbale yolowa imodzi yasiliva yolemera masekeli 70, malinga ndi muyezo wa sekeli la kumalo oyera. Mbale ziwiri zonsezo zinali zodzaza ndi ufa wosalala wothira mafuta, wa nsembe yambewu.
-