Ekisodo 16:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Choncho Yehova anauza Mose kuti: “Kodi anthu inu mudzakanabe kusunga malamulo ndi malangizo anga kufikira liti?+ Numeri 14:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 sadzaliona m’pang’ono pomwe dziko limene ndinalumbirira makolo awo. Ndithudi, onse amene sakundipatsa ulemu, sadzaliona dzikolo.+
28 Choncho Yehova anauza Mose kuti: “Kodi anthu inu mudzakanabe kusunga malamulo ndi malangizo anga kufikira liti?+
23 sadzaliona m’pang’ono pomwe dziko limene ndinalumbirira makolo awo. Ndithudi, onse amene sakundipatsa ulemu, sadzaliona dzikolo.+