Ekisodo 39:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Chotero ntchito yonse ya chihema chopatulika, kapena kuti chihema chokumanako, inatha, chifukwa ana a Isiraeli anachita zonse monga mmene Yehova analamulira Mose.+ Anachitadi momwemo.
32 Chotero ntchito yonse ya chihema chopatulika, kapena kuti chihema chokumanako, inatha, chifukwa ana a Isiraeli anachita zonse monga mmene Yehova analamulira Mose.+ Anachitadi momwemo.