Numeri 7:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Amene anapereka zopereka zake pa tsiku loyamba anali Naasoni,+ mwana wa Aminadabu, wa fuko la Yuda. Numeri 10:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Choncho, a m’chigawo cha mafuko atatu cha ana a Yuda ndiwo anayamba kunyamuka m’magulu awo.+ Mtsogoleri wa asilikali awo anali Naasoni,+ mwana wa Aminadabu. Rute 4:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Aminadabu+ anabereka Naasoni,+ Naasoni anabereka Salimoni, 1 Mbiri 2:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ramu anabereka Aminadabu, Aminadabu+ anabereka Naasoni+ mtsogoleri wa ana a Yuda. Mateyu 1:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ramu anabereka Aminadabu.Aminadabu anabereka Naasoni.+Naasoni anabereka Salimoni.+
12 Amene anapereka zopereka zake pa tsiku loyamba anali Naasoni,+ mwana wa Aminadabu, wa fuko la Yuda.
14 Choncho, a m’chigawo cha mafuko atatu cha ana a Yuda ndiwo anayamba kunyamuka m’magulu awo.+ Mtsogoleri wa asilikali awo anali Naasoni,+ mwana wa Aminadabu.