Numeri 32:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Yehova anawakwiyira koopsa Aisiraeli ndipo anawachititsa kuzungulira m’chipululu zaka 40,+ mpaka m’badwo wonse wochita zoipa pamaso pa Yehova utatha.+ Yoswa 14:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Yehova wandisunga ndi moyo+ monga mmene analonjezera.+ Tsopano padutsa zaka 45 kuchokera pamene Yehova analonjeza Mose, pa nthawi imene Aisiraeli anali m’chipululu,+ ndipo lero ndili ndi zaka 85.
13 Yehova anawakwiyira koopsa Aisiraeli ndipo anawachititsa kuzungulira m’chipululu zaka 40,+ mpaka m’badwo wonse wochita zoipa pamaso pa Yehova utatha.+
10 Yehova wandisunga ndi moyo+ monga mmene analonjezera.+ Tsopano padutsa zaka 45 kuchokera pamene Yehova analonjeza Mose, pa nthawi imene Aisiraeli anali m’chipululu,+ ndipo lero ndili ndi zaka 85.