Numeri 1:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 kuchokera ku fuko la Zebuloni,+ Eliyabu+ mwana wa Heloni. Numeri 7:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Pa tsiku lachitatu panali mtsogoleri wa ana a Zebuloni, Eliyabu+ mwana wa Heloni. Numeri 10:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ndipo mtsogoleri wa asilikali a fuko la ana a Zebuloni anali Eliyabu, mwana wa Heloni.+