Numeri 1:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 kuchokera ku fuko la Simiyoni,+ Selumiyeli+ mwana wa Zurisadai, Numeri 7:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Pa tsiku lachisanu panali mtsogoleri wa ana a Simiyoni, Selumiyeli+ mwana wa Zurisadai. Numeri 10:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Mtsogoleri wa asilikali a fuko la ana a Simiyoni+ anali Selumiyeli,+ mwana wa Zurisadai.