Numeri 12:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Tsopano Yehova anatsika mumtambo woima njo ngati chipilala+ n’kuima pakhomo la chihema chokumanako, ndipo anaitana Aroni ndi Miriamu. Pamenepo iwo anayandikira kumeneko. Numeri 14:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Koma khamu lonselo linayamba kunena zoti liwaponye miyala.+ Kenako, ulemerero wa Yehova unaonekera kwa ana a Isiraeli onse pamwamba pa chihema chokumanako.+
5 Tsopano Yehova anatsika mumtambo woima njo ngati chipilala+ n’kuima pakhomo la chihema chokumanako, ndipo anaitana Aroni ndi Miriamu. Pamenepo iwo anayandikira kumeneko.
10 Koma khamu lonselo linayamba kunena zoti liwaponye miyala.+ Kenako, ulemerero wa Yehova unaonekera kwa ana a Isiraeli onse pamwamba pa chihema chokumanako.+