-
Levitiko 27:28Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
28 “‘Ngati munthu watenga munthu mnzake, nyama kapena munda wake n’kuupatula kuti ukhale woyera kwa Yehova kwamuyaya,* kapena akapereka munthuyo, nyama kapena munda kwa Mulungu kuti auwononge,+ sungagulitsidwe kapena kuwomboledwa.+ Munthu, nyama kapena munda umenewo ndi wopatulika koposa. Zimenezi ndi za Yehova.
-
-
Numeri 18:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Mphatso zonse za ana a Isiraeli, limodzi ndi nsembe zawo zonse zoweyula*+ zimene azipereka monga zopereka zawo,+ zizikhala zako. Ndazipereka kwa iwe ndi kwa ana ako aamuna, limodzi ndi ana ako aakazi.+ Zikhale gawo lanu mpaka kalekale. Aliyense wa m’nyumba yako amene ndi wosadetsedwa azidya nawo.+
-