Levitiko 20:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 “‘Mwamuna kapena mkazi amene amalankhula ndi mizimu kapena amene amalosera zam’tsogolo+ aziphedwa ndithu.+ Aziphedwa mwa kuponyedwa miyala. Mlandu wa magazi awo ukhale wa iwo eni.’”+ 1 Mbiri 10:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Choncho Sauli anafa chifukwa cha kusakhulupirika kwake popeza anachita zosakhulupirika+ kwa Yehova. Iye sanasunge mawu a Yehova komanso anapita kukafunsa kwa wolankhula ndi mizimu.+
27 “‘Mwamuna kapena mkazi amene amalankhula ndi mizimu kapena amene amalosera zam’tsogolo+ aziphedwa ndithu.+ Aziphedwa mwa kuponyedwa miyala. Mlandu wa magazi awo ukhale wa iwo eni.’”+
13 Choncho Sauli anafa chifukwa cha kusakhulupirika kwake popeza anachita zosakhulupirika+ kwa Yehova. Iye sanasunge mawu a Yehova komanso anapita kukafunsa kwa wolankhula ndi mizimu.+