Deuteronomo 13:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 ndipo chizindikiro kapena chodabwitsa chimenecho chachitikadi,+ chimene anachita ponena kuti, ‘Tiyeni titsatire milungu ina imene simunaidziwe, ndipo tiitumikire,’ 1 Mafumu 18:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Tsopano tumizani uthenga ndipo musonkhanitse Aisiraeli onse kwa ine paphiri la Karimeli.+ Musonkhanitsenso aneneri 450 a Baala+ ndi aneneri 400 a mzati wopatulika,+ amene amadya patebulo la Yezebeli.”+ Yeremiya 23:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 “Ndaona zosayenera mwa aneneri a ku Samariya.+ Iwo atumikira ngati aneneri a Baala+ ndipo asocheretsa anthu anga, Aisiraeli.+
2 ndipo chizindikiro kapena chodabwitsa chimenecho chachitikadi,+ chimene anachita ponena kuti, ‘Tiyeni titsatire milungu ina imene simunaidziwe, ndipo tiitumikire,’
19 Tsopano tumizani uthenga ndipo musonkhanitse Aisiraeli onse kwa ine paphiri la Karimeli.+ Musonkhanitsenso aneneri 450 a Baala+ ndi aneneri 400 a mzati wopatulika,+ amene amadya patebulo la Yezebeli.”+
13 “Ndaona zosayenera mwa aneneri a ku Samariya.+ Iwo atumikira ngati aneneri a Baala+ ndipo asocheretsa anthu anga, Aisiraeli.+