Yoswa 11:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Choncho mafumuwo pamodzi ndi magulu awo onse ankhondo ananyamuka. Anali anthu ambiri, kuchuluka kwawo ngati mchenga wa m’mphepete mwa nyanja.+ Ndipo anali ndi mahatchi*+ ambiri zedi komanso magaleta* ankhondo.
4 Choncho mafumuwo pamodzi ndi magulu awo onse ankhondo ananyamuka. Anali anthu ambiri, kuchuluka kwawo ngati mchenga wa m’mphepete mwa nyanja.+ Ndipo anali ndi mahatchi*+ ambiri zedi komanso magaleta* ankhondo.