Numeri 15:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 “Lankhula ndi ana a Isiraeli, uwauze kuti azisokerera mphonje m’mphepete mwa zovala zawo, ku mibadwo yawo yonse. Azisokereranso chingwe cha buluu pamwamba pa mphonje za zovalazo.+ Mateyu 23:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Zonse zimene amachita, amazichita kuti anthu awaone.+ Iwo amakulitsa timapukusi tokhala ndi malemba+ timene amavala monga zodzitetezera, ndipo amakulitsanso ulusi wopota wa m’mphepete+ mwa zovala zawo.
38 “Lankhula ndi ana a Isiraeli, uwauze kuti azisokerera mphonje m’mphepete mwa zovala zawo, ku mibadwo yawo yonse. Azisokereranso chingwe cha buluu pamwamba pa mphonje za zovalazo.+
5 Zonse zimene amachita, amazichita kuti anthu awaone.+ Iwo amakulitsa timapukusi tokhala ndi malemba+ timene amavala monga zodzitetezera, ndipo amakulitsanso ulusi wopota wa m’mphepete+ mwa zovala zawo.