Genesis 37:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Tsopano amuna amalonda achimidiyani+ aja anali kudutsa mumsewu. Pamenepo abale a Yosefe anamutulutsa m’chitsimemo+ n’kumugulitsa kwa Aisimaeliwo. Anamugulitsa ndalama zasiliva 20,+ ndipo iwo anapita naye ku Iguputo.
28 Tsopano amuna amalonda achimidiyani+ aja anali kudutsa mumsewu. Pamenepo abale a Yosefe anamutulutsa m’chitsimemo+ n’kumugulitsa kwa Aisimaeliwo. Anamugulitsa ndalama zasiliva 20,+ ndipo iwo anapita naye ku Iguputo.