Yakobo 4:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Chotero, ngati munthu akudziwa kuchita chabwino koma sakuchichita,+ akuchimwa.+