Deuteronomo 16:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Uzitsatira chilungamo.+ Ndithudi uzitsatira chilungamo kuti ukhale ndi moyo ndi kukatengadi dziko limene Yehova Mulungu wako akukupatsa.+
20 Uzitsatira chilungamo.+ Ndithudi uzitsatira chilungamo kuti ukhale ndi moyo ndi kukatengadi dziko limene Yehova Mulungu wako akukupatsa.+