Yesaya 49:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Kodi mayi angaiwale mwana wake woyamwa, osamvera chisoni mwana wochokera m’mimba mwake?+ Ngakhale amayi amenewa akhoza kuiwala,+ koma ine sindidzakuiwala.+
15 Kodi mayi angaiwale mwana wake woyamwa, osamvera chisoni mwana wochokera m’mimba mwake?+ Ngakhale amayi amenewa akhoza kuiwala,+ koma ine sindidzakuiwala.+